6 Kenako ansembe anabweretsa likasa+ la pangano la Yehova kumalo ake,+ kuchipinda chamkati cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa, ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+
18 Anayezanso golide woyengedwa bwino wa guwa lansembe la zofukiza+ malinga ndi kulemera kwake, ndiponso golide wa chifaniziro cha galeta,+ kutanthauza akerubi+ agolide otambasula mapiko awo kuphimba likasa la pangano la Yehova.
7 Kenako ansembe anabweretsa likasa la pangano la Yehova kumalo ake, kuchipinda chamkati+ cha nyumbayo, Malo Oyera Koposa,+ ndipo analiika pansi pa mapiko a akerubi.+