7 Ndiyeno ndinauzanso mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, lolani kuti ndipatsidwe makalata+ okasonyeza kwa abwanamkubwa+ a tsidya lina la Mtsinje,*+ kuti akandilole kudutsa ndi kukafika ku Yuda.
7 Kenako Melatiya Mgibeoni+ ndi Yadoni Mmeronoti+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Yoyada ndi Mesulamu analekezera. Amenewa anali amuna a ku Gibeoni+ ndi Mizipa+ amene anali pansi pa ulamuliro wa bwanamkubwa+ wa kutsidya la Mtsinje.+