Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 24:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Iwonso anachita maere+ mofanana ndi mmene abale awo, ana a Aroni, anachitira pamaso pa Davide mfumu, Zadoki, Ahimeleki, ndiponso pamaso pa atsogoleri a nyumba za makolo za ansembe ndi za Alevi. Nyumba ya makolo+ ya wamkulu inali chimodzimodzi ndi nyumba ya makolo ya wamng’ono.

  • Ezara 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu amene anachokera ku ukapolowo+ anatsatira dongosolo limenelo, ndipo wansembe Ezara ndi amuna onse amene anali atsogoleri a nyumba za makolo awo,+ omwe anachita kuwatchula mayina awo, anachoka pakati pa anthuwo n’kukakhala pansi kuti afufuze nkhaniyo,+ kuyambira pa tsiku loyamba la mwezi wa 10.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena