-
Esitere 9:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Anatumiza makalatawo kuti atsimikizire kuti pa nthawi yoikidwiratu, Ayuda onse ndi ana awo azichita chikondwerero cha Purimu monga mmene Moredekai Myuda ndi Mfumukazi Esitere anawalamulira.+ Anawakumbutsanso lamulo limene iwo ndi ana awo+ anadziikira kuti adzasala kudya+ komanso kuti adzapemphera kwa Mulungu.+
-