Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma oipa sali choncho.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo.+ Salimo 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu oipa+ adzapita ku Manda,+Ngakhalenso anthu onse a mitundu ina amene aiwala Mulungu.+ Salimo 52:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu adzakupasula kosatha.+Adzakugwetsa ndi kukukokera kunja kwa hema wako,+Ndipo adzakuzula ndithu m’dziko la anthu amoyo.+ [Seʹlah.] Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
5 Mulungu adzakupasula kosatha.+Adzakugwetsa ndi kukukokera kunja kwa hema wako,+Ndipo adzakuzula ndithu m’dziko la anthu amoyo.+ [Seʹlah.]
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+