Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova anauzanso Mose kuti: “Ndawayang’ana anthu amenewa, ndipo ndaona kuti ndi anthu ouma khosi.+

  • 2 Mbiri 30:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano musaumitse khosi lanu+ ngati mmene anachitira makolo anu. Gonjerani Yehova,+ pitani kunyumba yake yopatulika+ imene waiyeretsa+ mpaka kalekale. Tumikirani+ Yehova Mulungu wanu kuti mkwiyo wake umene wakuyakirani+ ukuchokereni.

  • Miyambo 29:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Munthu wodzudzulidwa kawirikawiri+ koma amene amaumitsa khosi lake,+ adzathyoledwa mwadzidzidzi ndipo akadzatero sadzachira.+

  • Machitidwe 7:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+

  • Yuda 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu amenewa ndi okonda kung’ung’udza,+ okonda kudandaula za moyo wawo, ongotsatira zilakolako zawo,+ ndipo amalankhula modzitukumula.+ Amatamandanso anthu ena+ n’cholinga choti apezepo phindu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena