Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iweyo ukayenda+ pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, yemwe anali ndi mtima wosagawanika+ ndipo anayenda mowongoka,+ ukachita mogwirizana ndi zonse zimene ndinakulamula,+ komanso ukasunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+

  • 1 Mafumu 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamene iye anali kukalamba,+ akazi ake anali atapotoza+ mtima wake moti iye anali kutsatira milungu ina.+ Sanatumikire Yehova Mulungu wake ndi mtima wathunthu+ monga mmene anachitira Davide bambo ake.

  • Salimo 78:72
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 72 Iye anayamba kuwaweta malinga ndi mtima wake wosagawanika,+

      Ndipo anayamba kuwatsogolera mwaluso.+

  • Yesaya 38:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye anapemphera kuti: “Ndikukupemphani inu Yehova, chonde kumbukirani+ kuti ndinayenda+ pamaso panu mokhulupirika+ ndiponso ndi mtima wathunthu,+ komanso ndinachita zabwino pamaso panu.” Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena