Ekisodo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndine Yehova Mulungu wako,+ amene ndinakutulutsa m’dziko la Iguputo, m’nyumba yaukapolo.+ Deuteronomo 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Cholinga chake n’chakuti akukhazikitseni lero monga anthu ake+ ndi kuti akuonetseni kuti ndi Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani ndiponso monga mmene analumbirira makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+ Yoswa 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Tizitumikira Yehova Mulungu wathu ndi kumvera mawu ake!”+ Salimo 100:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+
13 Cholinga chake n’chakuti akukhazikitseni lero monga anthu ake+ ndi kuti akuonetseni kuti ndi Mulungu wanu,+ monga mmene anakulonjezerani ndiponso monga mmene analumbirira makolo anu, Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+
24 Ndiyeno anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Tizitumikira Yehova Mulungu wathu ndi kumvera mawu ake!”+
3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+