Deuteronomo 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Lero Yehova Mulungu wanu akukulamulani kutsatira malangizo ndi zigamulo+ zimenezi. Motero muzisunga ndi kutsatira zimenezi ndi mtima wanu+ wonse ndi moyo wanu wonse.+ 1 Mafumu 8:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Alozetse mtima wathu+ kwa iye kuti tiyende m’njira zake zonse+ ndi kusunga malamulo ake,+ malangizo ake,+ ndi zigamulo zake,+ zimene analamula makolo athu. Salimo 119:112 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 112 Ndatsimikiza mtima kutsatira malangizo anu,+Mpaka kalekale, ndithu kwa moyo wanga wonse.+
16 “Lero Yehova Mulungu wanu akukulamulani kutsatira malangizo ndi zigamulo+ zimenezi. Motero muzisunga ndi kutsatira zimenezi ndi mtima wanu+ wonse ndi moyo wanu wonse.+
58 Alozetse mtima wathu+ kwa iye kuti tiyende m’njira zake zonse+ ndi kusunga malamulo ake,+ malangizo ake,+ ndi zigamulo zake,+ zimene analamula makolo athu.