Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] Miyambo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khulupirira Yehova ndi mtima wako wonse,+ ndipo usadalire luso lako lomvetsa zinthu.+ Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ 1 Petulo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 amene kudzera mwa iye, mukukhulupirira Mulungu,+ amene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kum’patsa ulemerero,+ kuti chikhulupiriro ndiponso chiyembekezo chanu zikhale mwa Mulungu.+
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
21 amene kudzera mwa iye, mukukhulupirira Mulungu,+ amene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kum’patsa ulemerero,+ kuti chikhulupiriro ndiponso chiyembekezo chanu zikhale mwa Mulungu.+