Miyambo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aliyense wopusa sayenera moyo wawofuwofu.+ Ndiye kuli bwanji kuti wantchito alamulire akalonga!+ Miyambo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Monga chipale chofewa m’chilimwe ndiponso mvula pa nthawi yokolola,+ momwemonso ulemerero suyenerera munthu wopusa.+
26 Monga chipale chofewa m’chilimwe ndiponso mvula pa nthawi yokolola,+ momwemonso ulemerero suyenerera munthu wopusa.+