Yobu 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amapatutsa osauka panjira,+Ndipo pa nthawi yomweyo ozunzika a padziko lapansi amakhala atabisala. Miyambo 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olungama akamasangalala+ zimakhala bwino kwambiri, koma anthu oipa akamalamulira, munthu amadzisintha maonekedwe.+
12 Anthu olungama akamasangalala+ zimakhala bwino kwambiri, koma anthu oipa akamalamulira, munthu amadzisintha maonekedwe.+