Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo anthu onse ndi akulu amene anali pachipata anayankha kuti: “Ndife mboni! Yehova adalitse mkazi amene akulowa m’nyumba mwako kuti akhale ngati Rakele+ ndi Leya,+ akazi amene anabereka ana a nyumba ya Isiraeli.+ Uonetse kulemekezeka kwako mu Efurata+ ndi kudzipangira dzina m’Betelehemu.+

  • 1 Mafumu 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho Bati-seba anapita kwa Mfumu Solomo kuti akauze mfumuyo zofuna za Adoniya.+ Nthawi yomweyo mfumu inaimirira+ kuti ikumane naye ndipo inamuweramira.+ Kenako inakhala pampando wake wachifumu n’kuitanitsa mpando wina ndipo inauika kumbali yake yakumanja kuti amayi a mfumu akhalepo.+

  • 2 Timoteyo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti ndikukumbukira chikhulupiriro+ chopanda chinyengo+ chimene uli nacho, chimene chinayamba kukhazikika mwa agogo ako aakazi a Loisi, ndi mayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti chilinso mwa iwe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena