Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 39:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mbuye wa mnyamatayo atamva zimene mkazi wake anamuuza zakuti: “Wantchito wanu anachita zakutizakuti,” mkwiyo wake unayaka.+

  • Oweruza 20:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+

  • Oweruza 20:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyetu tipatseni amunawo,+ anthu opanda pakewo,+ amene ali mu Gibeya,+ kuti tiwaphe+ ndi kuchotsa choipachi mu Isiraeli.”+ Koma ana a Benjamini sanafune kumvera mawu a abale awo, ana a Isiraeli.+

  • Nyimbo ya Solomo 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Undiike pamtima pako ngati chidindo,+ ndiponso undiike ngati chidindo padzanja lako, chifukwa chikondi n’champhamvu ngati imfa.+ Mofanana ndi Manda,* chikondi sichigonja ndipo chimafuna kudzipereka ndi mtima wonse.+ Kuyaka kwake kuli ngati kuyaka kwa moto. Chikondicho ndi lawi la Ya.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena