Ekisodo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka.+ Amunanu musayandikire akazi anu.”*+ Miyambo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero pali chifukwa chanji choti usangalalire ndi mkazi wachilendo mwana wanga, kapena choti ukumbatirire chifuwa cha mkazi wina?+ Luka 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musatenge chikwama cha ndalama, thumba la chakudya,+ kapena nsapato. Ndipo musamachedwe mukamapereka moni panjira.+
15 Kenako anauza anthuwo kuti: “Pofika tsiku lachitatu mukhale okonzeka.+ Amunanu musayandikire akazi anu.”*+
20 Chotero pali chifukwa chanji choti usangalalire ndi mkazi wachilendo mwana wanga, kapena choti ukumbatirire chifuwa cha mkazi wina?+
4 Musatenge chikwama cha ndalama, thumba la chakudya,+ kapena nsapato. Ndipo musamachedwe mukamapereka moni panjira.+