Nyimbo ya Solomo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ndiwe wokongola kwabasi, wokondedwa wanga.+ Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa.”+ Afilipi 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+ 1 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Khalani ndi khalidwe labwino pakati pa anthu a m’dzikoli,+ kuti pamene akukunenerani monga anthu ochita zoipa, pa mapeto pake iwo pokhala mboni zimene zikuona ndi maso zochita zanu zabwino,+ adzatamande Mulungu m’tsiku lake loyendera.+
15 “Ndiwe wokongola kwabasi, wokondedwa wanga.+ Ndiwe chiphadzuwa. Maso ako ali ngati maso a njiwa.”+
15 kuti mukhale opanda chifukwa chokunenezani nacho ndiponso osalakwa.+ Mukhale ana a Mulungu opanda chilema+ pakati pa m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota,+ umene mukuwala pakati pawo monga zounikira m’dzikoli.+
12 Khalani ndi khalidwe labwino pakati pa anthu a m’dzikoli,+ kuti pamene akukunenerani monga anthu ochita zoipa, pa mapeto pake iwo pokhala mboni zimene zikuona ndi maso zochita zanu zabwino,+ adzatamande Mulungu m’tsiku lake loyendera.+