Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+

      Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+

  • Salimo 72:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+

      Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Salimo 86:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+

      Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+

      Ndi kulemekeza dzina lanu.+

  • Hagai 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Ndigwedeza mitundu yonse ya anthu, ndipo zinthu zamtengo wapatali zochokera ku mitundu yonse ya anthu zidzalowa m’nyumba imeneyi.+ Ine ndidzadzaza nyumbayi ndi ulemerero,’+ watero Yehova wa makamu.

  • Malaki 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Mitundu ina yonse ya anthu idzakutchani odala,+ pakuti mudzakhala dziko losangalatsa,”+ watero Yehova wa makamu.

  • Chivumbulutso 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena