Salimo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Psompsonani mwanayo+ kuopera kuti Mulungu angakwiye,Ndipo mungawonongeke ndi kuchotsedwa panjirayo.+Pakuti mkwiyo wake umatha kuyaka mofulumira.+Odala ndi onse amene akuthawira kwa iye.+ Yesaya 52:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+ Yesaya 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu ya anthu idzatsata kuwala kwako,+ ndipo mafumu+ adzatsata kunyezimira kwako.+
12 Psompsonani mwanayo+ kuopera kuti Mulungu angakwiye,Ndipo mungawonongeke ndi kuchotsedwa panjirayo.+Pakuti mkwiyo wake umatha kuyaka mofulumira.+Odala ndi onse amene akuthawira kwa iye.+
15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+