Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ndipo mu ukulu wanu wopambana mumagwetsa otsutsana nanu.+

      Mumatulutsa mkwiyo wanu woyaka moto, ndipo umanyeketsa otsutsana nanu ngati mapesi.+

  • Yoweli 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Amadumphadumpha ndipo amachita mkokomo ngati magaleta oyenda pamwamba pa mapiri+ ndiponso ngati moto walawilawi umene ukutentha mapesi.+ Iwo ali ngati anthu amphamvu amene afola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+

  • Nahumu 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ngakhale kuti iwo alukanalukana ngati minga+ ndipo aledzera ngati kuti amwa mowa,+ adzatenthedwa ngati mapesi ouma.+

  • Malaki 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ng’anjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi.+ Tsiku limene likubweralo lidzawanyeketsa moti pa iwo sipadzatsala mizu kapena nthambi,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena