Yobu 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu sadziwa mtengo wake,+Ndipo nzeru sizipezeka m’dziko la amoyo. Salimo 116:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzayenda+ pamaso pa Yehova m’dziko la anthu amoyo.+ Mlaliki 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+ Yesaya 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.
5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+
11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.