Salimo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mbewu idzamutumikira.+Adzalengeza za Yehova ku m’badwo wotsatira.+ Salimo 110:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+ Yesaya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+ 1 Akorinto 15:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zinachita kulembedwa kuti: “Munthu woyambirira, Adamu, anakhala munthu wamoyo.”+ Adamu womalizira anakhala mzimu+ wopatsa moyo.+ Aheberi 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso pamene akunena kuti: “Ndidzadalira iye.”+ Ndi kutinso: “Taonani! Ine ndi ana amene Yehova anandipatsa.”+
3 Anthu ako+ adzadzipereka mofunitsitsa+ pa tsiku limene udzatsogolera asilikali ako kunkhondo.+Wadzikongoletsa ndi ulemerero,+Ndipo gulu la achinyamata amene ali ngati mame a m’bandakucha lili pamodzi ndi iwe.+
6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+
45 Zinachita kulembedwa kuti: “Munthu woyambirira, Adamu, anakhala munthu wamoyo.”+ Adamu womalizira anakhala mzimu+ wopatsa moyo.+
13 Komanso pamene akunena kuti: “Ndidzadalira iye.”+ Ndi kutinso: “Taonani! Ine ndi ana amene Yehova anandipatsa.”+