Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 18:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Inu mudzandipulumutsa kwa anthu a mtundu wanga onditola zifukwa.+

      Mudzandiika kukhala mtsogoleri wa mitundu yonse.+

      Anthu amene sindikuwadziwa adzanditumikira.+

  • Yesaya 56:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, amene akusonkhanitsa pamodzi Aisiraeli omwe anabalalitsidwa,+ ndi akuti: “Ine ndidzamusonkhanitsiranso anthu ena kuwonjezera pa anthu ake amene anasonkhanitsidwa kale.”+

  • Machitidwe 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Sumeoni+ wafotokoza bwino mmene Mulungu anacheukira anthu a mitundu ina kwa nthawi yoyamba, kuti mwa iwo atengemo anthu odziwika ndi dzina lake.+

  • Aroma 11:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngati nthambi zina zinadulidwa, koma iwe ngakhale kuti ndiwe nthambi ya mtengo wa maolivi wam’tchire, unalumikizidwa pakati pa nthambi zotsala+ ndipo unayamba kugawana nawo muzu wamafuta+ wa mtengo wa maoliviwo,+

  • Aefeso 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chotero nthawi zonse muzikumbukira kuti poyamba munali anthu a mitundu ina mwakuthupi.+ Anthu otchedwa “odulidwa,” amene anadulidwa mwakuthupi ndi manja,+ anali kukutchani “osadulidwa.”

  • Chivumbulutso 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo anapitirizabe kufuula ndi mawu okweza, kuti: “Chipulumutso chathu chachokera kwa Mulungu wathu,+ amene wakhala pampando wachifumu,+ ndi kwa Mwanawankhosa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena