Yesaya 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ine, Yehova Mulungu wako, ndagwira dzanja lako lamanja.+ Ine amene ndikukuuza kuti, ‘Usachite mantha.+ Ineyo ndikuthandiza.’+ Yesaya 43:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Usachite mantha chifukwa ine ndili nawe.+ Ndidzabweretsa mbewu yako kuchokera kotulukira dzuwa, ndipo ndidzakusonkhanitsani pamodzi kuchokera kolowera dzuwa.+ Yesaya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha.
13 Pakuti ine, Yehova Mulungu wako, ndagwira dzanja lako lamanja.+ Ine amene ndikukuuza kuti, ‘Usachite mantha.+ Ineyo ndikuthandiza.’+
5 “Usachite mantha chifukwa ine ndili nawe.+ Ndidzabweretsa mbewu yako kuchokera kotulukira dzuwa, ndipo ndidzakusonkhanitsani pamodzi kuchokera kolowera dzuwa.+
2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha.