2 Mafumu 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zitatero, anthu onse, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu ndi akuluakulu a magulu ankhondo, ananyamuka n’kupita ku Iguputo,+ chifukwa anayamba kuopa Akasidi.+ Yesaya 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+ Yeremiya 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+ Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+
26 Zitatero, anthu onse, kuyambira wamng’ono mpaka wamkulu ndi akuluakulu a magulu ankhondo, ananyamuka n’kupita ku Iguputo,+ chifukwa anayamba kuopa Akasidi.+
2 amene akupita ku Iguputo+ osafunsira kwa ine,+ ndiponso amene akupita ku Iguputo kuti akapeze chitetezo kwa Farao ndi kukabisala mumthunzi wa Iguputo.+
14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+
7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+