Deuteronomo 28:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Yehova adzakubwezerani ku Iguputo pa zombo kudzera njira imene ndinakuuzani kuti, ‘Simudzaionanso.’+ Kumeneko mudzalakalaka kudzigulitsa kwa adani anu kuti mukhale akapolo aamuna ndi aakazi,+ koma sipadzakhala wokugulani.” Yeremiya 41:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo anakakhala kumalo ogona a Chimamu pafupi ndi Betelehemu+ ndi cholinga choti apitirize ulendo wawo kukalowa mu Iguputo.+ Yeremiya 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+ Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+
68 Yehova adzakubwezerani ku Iguputo pa zombo kudzera njira imene ndinakuuzani kuti, ‘Simudzaionanso.’+ Kumeneko mudzalakalaka kudzigulitsa kwa adani anu kuti mukhale akapolo aamuna ndi aakazi,+ koma sipadzakhala wokugulani.”
17 Iwo anakakhala kumalo ogona a Chimamu pafupi ndi Betelehemu+ ndi cholinga choti apitirize ulendo wawo kukalowa mu Iguputo.+
14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+
7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+