Numeri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Azitumikira inuyo ndi kugwira ntchito zawo za pachihema chonse.+ Koma asamayandikire zipangizo za m’malo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo mungafe.+ 2 Mafumu 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ansembe+ a malo okwezekawo sankabwera kuguwa lansembe la Yehova ku Yerusalemu. M’malomwake, ankadya mikate yopanda chofufumitsa+ pakati pa abale awo.
3 Azitumikira inuyo ndi kugwira ntchito zawo za pachihema chonse.+ Koma asamayandikire zipangizo za m’malo oyera, kapena kuyandikira guwa lansembe kuti iwowo kapena inuyo mungafe.+
9 Koma ansembe+ a malo okwezekawo sankabwera kuguwa lansembe la Yehova ku Yerusalemu. M’malomwake, ankadya mikate yopanda chofufumitsa+ pakati pa abale awo.