Yeremiya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma iwe umange m’chiuno+ ndipo upite kukawauza zonse zimene ndikulamule kuti ukawauze. Usagwidwe ndi mantha chifukwa cha iwo,+ kuopera kuti ndingakuchititse kugwidwa ndi mantha pamaso pawo. Ezekieli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikamalankhula nawe ndizikutsegula pakamwa. Ndiyeno iweyo uzikawauza kuti,+ ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.’ Wakumva amve,+ ndipo wosamva asamve, pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+
17 “Koma iwe umange m’chiuno+ ndipo upite kukawauza zonse zimene ndikulamule kuti ukawauze. Usagwidwe ndi mantha chifukwa cha iwo,+ kuopera kuti ndingakuchititse kugwidwa ndi mantha pamaso pawo.
27 Ndikamalankhula nawe ndizikutsegula pakamwa. Ndiyeno iweyo uzikawauza kuti,+ ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena.’ Wakumva amve,+ ndipo wosamva asamve, pakuti iwo ndi nyumba yopanduka.+