Hoseya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma iwe ubwerere kwa Mulungu wako.+ Usonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi chilungamo+ ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.+ Yoweli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+ Mateyu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali kulalikira kuti: “Lapani,+ pakuti ufumu wakumwamba wayandikira.”+
6 “Koma iwe ubwerere kwa Mulungu wako.+ Usonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi chilungamo+ ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.+
13 Ng’ambani mitima yanu+ osati zovala zanu+ ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu pakuti iye ndi wachisomo, wachifundo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Ndithu, iye adzakumverani chisoni chifukwa cha tsokalo.+