1 Mbiri 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+ Yesaya 55:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Ine ndamupereka+ iye monga mboni+ kwa mitundu ya anthu,+ ndiponso monga mtsogoleri+ ndi wolamulira+ wa mitundu ya anthu. Danieli 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye adzagonjetsa magulu ankhondo+ okhala ngati madzi osefukira, ndipo magulu ankhondowo adzawonongedwa.+ Mtsogoleri+ wa pangano+ nayenso+ adzawonongedwa. Mateyu 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamatchedwe ‘atsogoleri,’+ pakuti Mtsogoleri wanu ndi mmodzi, Khristu. Yohane 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Natanayeli anamuyankha kuti: “Rabi, ndinudi Mwana wa Mulungu,+ ndinu Mfumu+ ya Isiraeli.”
2 Chifukwa chakuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa abale ake, mwa iye munachokera mtsogoleri,+ koma udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.+
4 Taonani! Ine ndamupereka+ iye monga mboni+ kwa mitundu ya anthu,+ ndiponso monga mtsogoleri+ ndi wolamulira+ wa mitundu ya anthu.
22 Iye adzagonjetsa magulu ankhondo+ okhala ngati madzi osefukira, ndipo magulu ankhondowo adzawonongedwa.+ Mtsogoleri+ wa pangano+ nayenso+ adzawonongedwa.