Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 komanso m’chipululu,+ kumene munaona mmene Yehova Mulungu wanu anakunyamulirani.+ M’njira yonse imene munayenda anakunyamulani ngati mmene bambo amanyamulira mwana wake, mpaka kufika malo ano.’+

  • Deuteronomo 33:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+

      Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+

      Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+

      Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+

  • Yesaya 40:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye adzaweta gulu lake lankhosa ngati m’busa.+ Adzasonkhanitsa pamodzi ana a nkhosa ndi dzanja lake,+ ndipo adzawanyamulira pachifuwa pake.+ Nkhosa zoyamwitsa adzayenda nazo mosamala.+

  • Yesaya 46:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inu a nyumba ya Yakobo ndimvetsereni. Ndimvetsereni inu nonse otsala a m’nyumba ya Isiraeli,+ inu amene ndinakunyamulani kuyambira pamene munabadwa, ndiponso inu amene ndinakusamalirani kuyambira pamene munatuluka m’mimba.+

  • Yesaya 63:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena