Ezekieli 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘“Ndidzawapatsa munda wotchuka+ ndipo sadzafa ndi njala m’dzikomo.+ Mitundu ina ya anthu sidzawanyozanso.+ Ezekieli 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Ndidzathetsa nkhani zonyoza zimene anthu a mitundu ina amakunenerani.+ Mitundu ya anthu sidzakunyozaninso+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu okhala mwa inu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
29 “‘“Ndidzawapatsa munda wotchuka+ ndipo sadzafa ndi njala m’dzikomo.+ Mitundu ina ya anthu sidzawanyozanso.+
15 ‘Ndidzathetsa nkhani zonyoza zimene anthu a mitundu ina amakunenerani.+ Mitundu ya anthu sidzakunyozaninso+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu okhala mwa inu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”