Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Afilipi 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Sanatero ayi, koma anasiya zonse zimene anali nazo n’kukhala ngati kapolo,+ ndi kukhala wofanana ndi anthu.+

  • 1 Timoteyo 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndithudi, chinsinsi chopatulikachi+ chokhudza kukhala odzipereka kwa Mulungu n’chachikulu ndithu: ‘Iye anaonekera ngati munthu,+ anaonedwa kuti ndi wolungama pamene anali mzimu,+ anaonekera kwa angelo,+ analalikidwa kwa mitundu ya anthu,+ anthu padziko lapansi anamukhulupirira,+ ndiponso analandiridwa kumwamba mu ulemerero.’+

  • Aheberi 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chotero, popeza kuti “ana” amenewo onse ndi amagazi ndi mnofu, iyenso anakhala wamagazi ndi mnofu.+ Anachita izi kuti kudzera mu imfa yake,+ awononge+ Mdyerekezi,+ amene ali ndi njira yobweretsera imfa.+

  • 1 Yohane 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kuti tidziwe ngati mawu ali ouziridwa ndiponso ochokera kwa Mulungu,+ timadziwira izi: Mawuwo amavomereza zoti Yesu Khristu anabwera monga munthu.+

  • 2 Yohane 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 popeza anthu onyenga ambiri alowa m’dziko,+ amene amatsutsa zakuti kalero Yesu Khristu anabwera monga munthu.+ Amene amachita zimenezi ndi wonyenga+ uja ndiponso wokana Khristu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena