Salimo 18:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 N’chifukwa chake ndidzakutamandani, inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ Yesaya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’tsiku limenelo,+ padzakhala muzu wa Jese+ womwe udzaimirire ngati chizindikiro kwa anthu.+ Ngakhale anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awatsogolere,+ ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero.+ Yesaya 52:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+
49 N’chifukwa chake ndidzakutamandani, inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+
10 M’tsiku limenelo,+ padzakhala muzu wa Jese+ womwe udzaimirire ngati chizindikiro kwa anthu.+ Ngakhale anthu a mitundu ina adzatembenukira kwa iye kuti awatsogolere,+ ndipo malo ake okhalapo adzakhala aulemerero.+
15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+