Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo ndi amene achita zinthu zoipa.+

      Iwo si ana ake, ali ndi vuto ndi iwowo.+

      Iwo ndi mʼbadwo wopotoka maganizo komanso wachinyengo!+

  • Yesaya 65:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndatambasula manja anga tsiku lonse kwa anthu amakani,+

      Kwa anthu amene akuyenda mʼnjira yoipa,+

      Potsatira maganizo awo,+

  • Mateyu 17:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yesu anayankha kuti: “Inu mʼbadwo wopanda chikhulupiriro ndi wopotoka maganizo,+ kodi ndikhala nanube mpaka liti? Ndipitirize kukupirirani mpaka liti? Bwera nayeni kuno.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena