Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Panali mwamuna wina wa ku Ramatayimu-zofimu,*+ kudera lamapiri la Efuraimu,+ dzina lake Elikana.+ Iye anali mwana wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana wa Zufi, ndipo anali wa fuko la Efuraimu.

  • 1 Samueli 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Patapita nthawi, akulu onse a mu Isiraeli anasonkhana pamodzi nʼkupita kwa Samueli ku Rama.

  • 1 Samueli 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Davide anathawa nʼkukafika kwa Samueli ku Rama+ ndipo anafotokozera Samueli zonse zimene Sauli anamuchitira. Kenako Davide ndi Samueli anachoka nʼkukakhala ku Nayoti.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena