16Kenako Kora+ mwana wa Izara,+ mwana wa Kohati,+ mwana wa Levi,+ anagwirizana ndi adzukulu a Rubeni,+ omwe ndi Datani ndi Abiramu ana a Eliyabu,+ komanso Oni mwana wa Pelete, kuti aukire.
10 Zitatero, nthaka inangʼambika* nʼkuwameza. Koma Kora anafa pamene moto unapsereza amuna 250.+ Ndipo iwo anakhala chitsanzo chotichenjeza.+11 Koma ana a Kora sanafe.+