1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+
10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+