Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+ Salimo 145:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova amayangʼanira onse amene amamukonda,+Koma oipa onse adzawawononga.+
10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+