Salimo 37:39, 40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya mavuto.+ 40 Yehova adzawathandiza nʼkuwapulumutsa.+ Adzawalanditsa kwa oipa nʼkuwapulumutsa,Chifukwa athawira kwa iye.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawi yamavuto mundiitane.+ Ine ndidzakupulumutsani, ndipo inu mudzandilemekeza.”+
39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya mavuto.+ 40 Yehova adzawathandiza nʼkuwapulumutsa.+ Adzawalanditsa kwa oipa nʼkuwapulumutsa,Chifukwa athawira kwa iye.+