Salimo 132:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ansembe ake ndidzawaveka chipulumutso,+Ndipo okhulupirika ake adzafuula mosangalala.+ Yesaya 61:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzasangalala kwambiri mwa Yehova. Ndidzasangalala mwa Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse.+ Chifukwa iye wandiveka zovala zachipulumutso.+Wandiveka mkanjo wa chilungamo,*Ngati mkwati amene wavala nduwira yofanana ndi ya wansembe,+Ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.
10 Ndidzasangalala kwambiri mwa Yehova. Ndidzasangalala mwa Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse.+ Chifukwa iye wandiveka zovala zachipulumutso.+Wandiveka mkanjo wa chilungamo,*Ngati mkwati amene wavala nduwira yofanana ndi ya wansembe,+Ndiponso ngati mkwatibwi amene wavala zinthu zake zodzikongoletsera.