Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nditetezeni ngati mwana wa diso lanu,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu.+ Salimo 121:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova adzakuteteza ku zinthu zonse zimene zingakuvulaze.+ Iye adzateteza moyo wako.+