Salimo 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndithudi, palibe anthu amene amayembekezera inu amene adzachite manyazi.+Koma amene adzachite manyazi ndi anthu amene amachita zachinyengo popanda chifukwa.+ Salimo 62:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndithudi, ndikuyembekezera Mulungu modekha*+Chifukwa chiyembekezo changa chimachokera kwa iye.+
3 Ndithudi, palibe anthu amene amayembekezera inu amene adzachite manyazi.+Koma amene adzachite manyazi ndi anthu amene amachita zachinyengo popanda chifukwa.+