Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 63:11-13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo anakumbukira masiku akale,

      Masiku a Mose mtumiki wake,

      Ndipo anafunsa kuti: “Kodi amene anawatulutsa mʼnyanja+ pamodzi ndi abusa a anthu ake+ uja ali kuti?

      Ali kuti amene anaika mzimu wake woyera mwa iye?+

      12 Ali kuti amene anachititsa mkono wake waulemerero kuti upite ndi dzanja lamanja la Mose,+

      Amene anagawanitsa madzi pamaso pawo+

      Kuti adzipangire dzina lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+

      13 Amene anawachititsa kuti adutse pamadzi amphamvu*

      Moti anayenda osapunthwa,

      Mofanana ndi hatchi mʼchipululu?*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena