Salimo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+ Salimo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.+