Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.

      Ndi ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mʼbadwo wa makolo ake?*

      Popeza iye anadulidwa mʼdziko la anthu amoyo.+

      Iye anakwapulidwa* chifukwa cha zolakwa za anthu anga.+

  • Yesaya 53:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, ndidzamupatsa gawo pamodzi ndi ambiri,

      Ndipo iye adzagawana ndi amphamvu katundu amene alanda kunkhondo,

      Chifukwa anapereka moyo wake*+

      Ndipo anaikidwa mʼgulu la anthu ochimwa.+

      Ananyamula tchimo la anthu ambiri+

      Ndipo analowererapo kuti athandize anthu ochimwa.+

  • Mateyu 26:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Inu mukudziwa kuti Pasika achitika pakangopita masiku awiri+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+

  • Luka 24:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kodi sikunali koyenera kuti Khristu amve zowawa zonsezi+ nʼkulowa mu ulemerero wake?”+

  • 1 Akorinto 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pa zinthu zoyambirira zimene ndinakuphunzitsani, zomwenso ineyo ndinalandira, panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, mogwirizana ndi Malemba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena