Machitidwe 7:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Iwo anapha anthu amene analengezeratu za kubwera kwa wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndiponso kumupha.+ Aheberi 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi ndiperekenso zitsanzo zina? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide+ komanso Samueli+ ndi aneneri ena. Aheberi 11:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa, anadulidwa pakati, anaphedwa ndi lupanga+ ndiponso anayendayenda atavala zikopa za nkhosa ndi zikopa za mbuzi.+ Ankasowa zinthu, ankazunzidwa+ komanso ankakumana ndi mavuto ena.+
52 Ndi mneneri uti amene makolo anuwo sanamuzunze?+ Iwo anapha anthu amene analengezeratu za kubwera kwa wolungamayo,+ amene inuyo munamupereka ndiponso kumupha.+
32 Kodi ndiperekenso zitsanzo zina? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide+ komanso Samueli+ ndi aneneri ena.
37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa, anadulidwa pakati, anaphedwa ndi lupanga+ ndiponso anayendayenda atavala zikopa za nkhosa ndi zikopa za mbuzi.+ Ankasowa zinthu, ankazunzidwa+ komanso ankakumana ndi mavuto ena.+