Aroma 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kondwerani chifukwa cha chiyembekezo. Muzipirira mavuto.+ Muzilimbikira kupemphera.+ Aefeso 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse. Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+ Akolose 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzilimbikira kupemphera.+ Mukhale maso pa nkhani ya kupemphera ndipo muziyamikira.+ 1 Atesalonika 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzipemphera nthawi zonse.+
18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse.
6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+