-
Akolose 2:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kuwonjezera pamenepo, ngakhale kuti munali akufa chifukwa cha machimo anu komanso chifukwa choti munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu.+ Mokoma mtima anatikhululukira machimo athu onse+ 14 ndipo anafafaniza Chilamulo+ chimene chinali ndi malamulo ambirimbiri+ omwe ankatitsutsa.+ Iye anachichotsa pochikhomerera pamtengo wozunzikirapo.*+
-