Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Chifukwa matupi oti akhoza kuwonongekawa adzasintha nʼkukhala oti sangawonongeke.+ Ndipo matupi oti angafewa adzasintha nʼkukhala oti sangafe.+

  • 1 Petulo 1:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Atamandike Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, yemwenso ndi Atate wake. Mulungu anatisonyeza chifundo chachikulu pamene anachititsa kuti tibadwenso mwatsopano+ nʼkukhala ndi chiyembekezo chodalirika.+ Zimenezi zinatheka chifukwa cha kuukitsidwa kwa Yesu Khristu.+ 4 Anachititsa kuti tibadwenso mwatsopano kuti tikhale ndi cholowa chosawonongeka, chosadetsedwa ndiponso chosasuluka.+ Cholowa chimenechi anakusungirani kumwamba.+

  • 1 Yohane 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Okondedwa, tsopano ndife ana a Mulungu,+ koma panopa sizinaonekerebe kuti tidzakhala otani.+ Tikudziwa kuti akadzaonekera, tidzakhala ngati iyeyo, chifukwa tidzamuona mmene alili.

  • Chivumbulutso 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Wosangalala komanso woyera ndi aliyense amene akuuka nawo pa kuuka koyamba.+ Imfa yachiwiri+ ilibe ulamuliro pa amenewa.+ Koma adzakhala ansembe+ a Mulungu ndi a Khristu, ndipo adzalamulira monga mafumu limodzi ndi Khristu zaka 1,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena