Ndandanda ya Mlungu wa September 28
MLUNGU WOYAMBIRA SEPTEMBER 28
Phunziro la Baibulo la Mpingo:
cl-CN mutu 26 ndime 16-23 ndi bokosi la patsamba 269
□ Sukulu ya Utumiki wa Mulungu:
Kuwerenga Baibulo: Numeri 33-36
Na. 1: Numeri 33:1-23
Na. 2: Tingauke kwa Akufa! (lr-CN mutu 35)
Na. 3: Kodi Ufumu wa Mulungu Umaposa Maboma a Anthu M’njira Ziti?
□ Msonkhano wa Utumiki:
Mph. 5: Zilengezo.
Mph. 10: Kugwiritsa Ntchito Mafanizo Pophunzitsa. Nkhani yochokera m’buku la Sukulu ya Utumiki, masamba 240-243.
Mph. 20: “Fufuzani Anthu Oyenerera.” Kambiranani mwa mafunso ndi mayankho. Funsani wofalitsa mmodzi kapena awiri amene amayesetsa kulalikira pogwiritsa ntchito njira zosiyanasiyana.